SITIKUCHITA BWINO CHIFUKWA TIKUNGOSEWERA KOYENDA | CHIGOGA

Eliza Bonongwe
0

 

Mkulu oyendetsa ntchito za timu ya FCB Nyasa Big Bullets Mr Albert Chigoga


Mkulu oyendetsa ntchito za timu ya FCB Nyasa Big Bullets Mr Albert Chigoga wadzuzula bungwe la SULOM pokanika kuyendetsa league ya chaka chino


Mwa zina Chigoga wati kulephera kusanja masewero okomera matimu onse ndiye gwero la kusachita bwino kwa matimu ena mongaso timu yawo ya Bullets


“We have played four consecutive away matches, spending two full weeks on the road and covering more than 2,600 kilometres,”


“Playing two away matches in a row is understandable, but four? That’s extreme. Meanwhile, our fellow contenders have five straight home games in the run-in. Where does that happen in world football?”


Izi zikusatira Kugonja Kwa timuyi pa Mzuzu Stadium ndi timu ya Moyale Baracks FC ndi zigoli ziwiri kwa chilowere.

Post a Comment

0 Comments
Post a Comment (0)
To Top