Ojiya aku 25 apambaza Mkulu Wina Kaamba kokhala Father Christmas Osauka

Eliza Bonongwe
0

Anyamata oitanila minibus ndi ma taxi ku Msungwi mu mzinda wa Lilongwe awowoza (booing and heckling) munthu amene anavala attire ya father Christmas komanso kunuthira fumbi ndikumuvulanso zomwe anavala zo ati chifukwa father Christmas samayenda wapansi. 


Anyamata wa anapanga izi uku akumunena munthu yi kuti zimene akupanga zi ndikunyozetsa gule chifukwa kudabwe kulibe attire ya father Christmas. 


Dera la Msungwi linapanga chidwi ndi izizi pomwe anthu ambiri anabwera kuzawonela mnyamata anavala za gather Christmas yi akumuvula. Anamusiya ndi jersey ya Manchester United komanso boxer wa orange yemwe anavala mkati ndikumuiza azipita.9

Post a Comment

0 Comments
Post a Comment (0)
To Top