Jetu ndi Zeze Akutulutsa Nyimbo ya Sopano M'mawa

Eliza Bonongwe
0
Jetu


M’modzi mwa oyimba  odziwika Bwino mdziko muno Jetu wati atulutsa Kanema wa tsopano mawa 8 koloko m’mawa.


Oyendetsa ntchito za Jetu (Manager) yemwe ndi mdzukulu wake Emmu Dee wauza Luntha Online kuti Kanema watsopanoyi “Osakwiya” wayimba ndi Katswiri wa chamba cha Amapiano Zeze.


“Tili mu nyengo ya zisangalalo ndiye Nyimbo Iyi ndi Mphatso ya khrisimasi ndi nyuwere kupita kwa a Malawi. Nyimbo imeneyi ivuta Muma pub”, watero Emmu Dee.


Zina mwa nyimbo zomwe Jetu anayimba ndi Pangoline, Wakalamba Wafuna, Chakwaza, Wayimanya.

Post a Comment

0 Comments
Post a Comment (0)
To Top