CHAMPIONS OF A SPERMATIC RACE and other poems by Hagai Magai

Malawi Heat
0


 CHAMPIONS OF A SPERMATIC RACE


Millions of sperms

Competed the race

And you won

 

Come here, sit down

The mathematics

Should scare you

 

A day earlier

Would have

been too soon

 

A day later

Was too late.

 

You won the first race

You can not lose

This second one.

 

Do you deny

The intersection

Was divine?

 

Do you doubt

You were made only for me

Only for me

 

 

DZIRA

Umuna ma million

Udatuluka nchiwuno

Mwa abambo ako

 

Kuthamangira ine.

Pamenepo Iwe nkuwina

Chimpikisanocho.

 

Sitimafunika tizidandaula

Chifukwa moyo

ndi mphatso

 

Tidawina kale

Nkhondo

 

REVELATION

 

Hagai Magai

 

Ndili mu mdimawo

Kusaka chakudya

Njala ya masiku asanu

Ndi anayi

 

Ndina peza chinthu cholankhula

"sankhapo chimodzi

 bowa

Kapena machesi"

 

Ndidafuna kudziwa

Kuti chidandilankhulacho

Chidali chani

 

Mawu ake

Sankamveka ngati amunthu

Koma a m'ngelo

Komanso kwinaku njala

Idali  pafupi kundipha

 

Koma chimati

"sankhapo chimodzi

 Machesi

Kapena chakudya?

Sankha  chakudya iwe

 upulumuke!"

 

Ndidasankha machesi

Nditayatsa

Ndidaona iwe.

 

 

 

 

 

 

 

Post a Comment

0 Comments
Post a Comment (0)
To Top